Danieli 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ponena za nyanga 10 zija, mu ufumuwo mudzatuluka mafumu 10. Pambuyo pa mafumu amenewa padzatulukanso mfumu ina imene idzakhale yosiyana ndi oyambawa ndipo idzagonjetsa mafumu atatu.+
24 Ponena za nyanga 10 zija, mu ufumuwo mudzatuluka mafumu 10. Pambuyo pa mafumu amenewa padzatulukanso mfumu ina imene idzakhale yosiyana ndi oyambawa ndipo idzagonjetsa mafumu atatu.+