Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 64:10, 11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mizinda yanu yoyera yasanduka chipululu.

      Ziyoni wasanduka chipululu,

      Ndipo Yerusalemu wasanduka bwinja.+

      11 Nyumba yathu yoyera* ndiponso yaulemerero,*

      Imene makolo athu ankakutamandiranimo,

      Yawotchedwa ndi moto,+

      Ndipo zinthu zathu zonse zimene tinkaziona kuti ndi zamtengo wapatali zasanduka mabwinja

  • Maliro 5:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chifukwa cha Phiri la Ziyoni limene lakhala bwinja+ ndipo tsopano nkhandwe zikuyendayenda mmenemo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena