Danieli 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mʼchaka chachitatu cha ulamuliro wa Mfumu Belisazara,+ ineyo Danieli ndinaona masomphenya pambuyo pa masomphenya amene ndinaona poyamba aja.+
8 Mʼchaka chachitatu cha ulamuliro wa Mfumu Belisazara,+ ineyo Danieli ndinaona masomphenya pambuyo pa masomphenya amene ndinaona poyamba aja.+