Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kenako ndinauza mfumu kuti: “Ngati zili bwino ndi inu mfumu, ndipo ngati mungandikomere mtima ine mtumiki wanu, munditumize ku Yuda, kumzinda umene makolo anga anaikidwako kuti ndikaumangenso.”+

  • Nehemiya 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Patapita nthawi, ndinafika ku Yerusalemu ndipo ndinakhala kumeneko masiku atatu.

  • Nehemiya 6:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Choncho ntchito yomanga mpanda inatha pa tsiku la 25 la mwezi wa Eluli* ndipo inatenga masiku 52.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena