Danieli 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mulungu woona anachititsa kuti anyamata* 4 amenewa akhale odziwa zinthu komanso ozindikira zinthu zonse zolembedwa ndipo anawapatsa nzeru. Danieli anamupatsa nzeru zoti azitha kumvetsa bwino masomphenya ndi maloto amtundu uliwonse.+ Danieli 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma kumwamba kuli Mulungu amene ndi Woulula zinsinsi,+ ndipo wakudziwitsani inu Mfumu Nebukadinezara zimene zidzachitike mʼmasiku otsiriza. Maloto anu komanso masomphenya amene munaona muli pabedi lanu ndi awa:
17 Mulungu woona anachititsa kuti anyamata* 4 amenewa akhale odziwa zinthu komanso ozindikira zinthu zonse zolembedwa ndipo anawapatsa nzeru. Danieli anamupatsa nzeru zoti azitha kumvetsa bwino masomphenya ndi maloto amtundu uliwonse.+
28 Koma kumwamba kuli Mulungu amene ndi Woulula zinsinsi,+ ndipo wakudziwitsani inu Mfumu Nebukadinezara zimene zidzachitike mʼmasiku otsiriza. Maloto anu komanso masomphenya amene munaona muli pabedi lanu ndi awa: