-
Danieli 2:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Pa nthawi imeneyo Danieli analankhula mwanzeru komanso mosamala kwambiri ndi Arioki mkulu wa asilikali olondera mfumu, amene anali atanyamuka kale kuti akaphe amuna anzeru a mʼBabulo.
-