Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 4:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 “Nthawi imeneyi itatha,+ ine Nebukadinezara ndinayangʼana kumwamba ndipo nzeru zanga zinabwerera. Ndinatamanda Wamʼmwambamwamba ndipo amene adzakhalepo mpaka kalekale ndinamutamanda ndi kumulemekeza, chifukwa ulamuliro wake udzakhalapo mpaka kalekale ndipo ufumu wake udzakhalapo kumibadwomibadwo.+

  • Chivumbulutso 4:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Nthawi zonse angelowo akamapereka ulemerero ndi ulemu ndiponso akamayamikira Mulungu amene wakhala pampando wachifumuyo, Amene adzakhale ndi moyo kwamuyaya,+

  • Chivumbulutso 10:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Iye analumbira mʼdzina la Mulungu amene adzakhale ndi moyo mpaka kalekale,+ amene analenga kumwamba ndi zinthu zonse zimene zili kumeneko, dziko lapansi ndi zinthu zonse zimene zili mmenemo komanso nyanja ndi zinthu zonse zimene zili mmenemo.+ Analumbira kuti: “Nthawi yodikira yatha.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena