Danieli 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mphamvu za mfumuyo zidzachuluka, koma si iye amene adzachititse zimenezi. Idzawononga zinthu zambiri moti idzadabwitsa anthu. Chilichonse chimene mfumuyo izidzachita chizidzaiyendera bwino. Idzawononga anthu amphamvu ndi anthu oyera.+
24 Mphamvu za mfumuyo zidzachuluka, koma si iye amene adzachititse zimenezi. Idzawononga zinthu zambiri moti idzadabwitsa anthu. Chilichonse chimene mfumuyo izidzachita chizidzaiyendera bwino. Idzawononga anthu amphamvu ndi anthu oyera.+