Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Choncho iye anabwera pafupi ndi pamene ine ndinaima. Koma atafika, ndinachita mantha kwambiri ndipo ndinagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yanga pansi. Ndiyeno anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, dziwa kuti masomphenyawa ndi okhudza nthawi yamapeto.”+

  • Danieli 8:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Zinthu zimene zanenedwa mʼmasomphenya zokhudza nsembe zamadzulo ndi zamʼmawa zija ndi zoona. Koma iweyo usunge masomphenyawo mwachinsinsi, chifukwa akunena zimene zidzachitike mʼtsogolo patapita masiku ambiri.”+

  • Danieli 10:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ine ndabwera kudzakuthandiza kuti umvetse zimene zidzachitikire anthu a mtundu wako mʼmasiku otsiriza,+ chifukwa masomphenyawa ndi okhudza zimene zidzachitike mʼtsogolo.”+

  • Danieli 12:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma iwe Danieli, sunga mawuwa mwachinsinsi ndipo umate bukuli mpaka nthawi yamapeto.+ Anthu ambiri adzaphunzira bukuli mokwanira* ndipo adzadziwa zinthu zambiri zoona.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena