Danieli 11:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ena mwa anthu ozindikirawo adzapunthwa. Zidzakhala choncho kuti ntchito yoyenga ichitike chifukwa cha iwowo ndiponso kuti anthu ozindikira atsukidwe ndi kuyeretsedwa+ mpaka nthawi ya mapeto, chifukwa mapetowo adzafika pa nthawi yake.
35 Ena mwa anthu ozindikirawo adzapunthwa. Zidzakhala choncho kuti ntchito yoyenga ichitike chifukwa cha iwowo ndiponso kuti anthu ozindikira atsukidwe ndi kuyeretsedwa+ mpaka nthawi ya mapeto, chifukwa mapetowo adzafika pa nthawi yake.