Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 111:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Chiyambi cha nzeru ndi kuopa Yehova.+

      ש [Sin]

      Onse otsatira malamulo ake amasonyeza kuti ndi ozindikira.+

      ת [Taw]

      Iye ayenera kutamandidwa mpaka kalekale.

  • Danieli 11:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Anthu ozindikira+ pakati pa anthuwo adzathandiza anthu ambiri kuti amvetse zinthu. Kwa masiku angapo iwo adzapunthwa chifukwa cha lupanga, malawi a moto, kutengedwa ukapolo komanso chifukwa cha kuwonongedwa kwa zinthu zawo.

  • Danieli 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Anthu ozindikira adzawala kwambiri ngati kuwala kwa kuthambo. Ndipo amene akuthandiza anthu ambiri kuti akhale olungama adzawala ngati nyenyezi mpaka muyaya.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena