Danieli 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nyangayo inadzitukumula ngakhale pamaso pa Kalonga wa gululo. Inachititsa kuti nsembe imene inkaperekedwa nthawi zonse kwa Kalongayo isamaperekedwenso ndipo malo opatulika amene iye anakhazikitsa anagwetsedwa.+
11 Nyangayo inadzitukumula ngakhale pamaso pa Kalonga wa gululo. Inachititsa kuti nsembe imene inkaperekedwa nthawi zonse kwa Kalongayo isamaperekedwenso ndipo malo opatulika amene iye anakhazikitsa anagwetsedwa.+