31 Ndiyeno magulu a asilikali ake adzachitapo kanthu ndipo adzaipitsa malo opatulika,+ malo okhala ndi mpanda wolimba kwambiri komanso adzachotsa nsembe zoyenera kuperekedwa nthawi zonse.+
Iwo adzaika pamalowo chinthu chonyansa chobweretsa chiwonongeko.+