Yeremiya 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yehova wanena kuti: “Kodi mawu anga safanana ndi moto?+ Kodi safanana ndi hamala imene imaphwanya thanthwe?”+
29 Yehova wanena kuti: “Kodi mawu anga safanana ndi moto?+ Kodi safanana ndi hamala imene imaphwanya thanthwe?”+