Ekisodo 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani mʼdziko la Iguputo, mʼnyumba yaukapolo.+ Hoseya 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma ine ndine Yehova Mulungu wako kuchokera pamene unali ku Iguputo.+Palibe Mulungu wina amene unkamudziwa kupatula ine.Palibenso mpulumutsi wina kupatula ine.+
4 Koma ine ndine Yehova Mulungu wako kuchokera pamene unali ku Iguputo.+Palibe Mulungu wina amene unkamudziwa kupatula ine.Palibenso mpulumutsi wina kupatula ine.+