Hoseya 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Zoipa zawo zonse zinachitikira ku Giligala,+ ndipo ndinadana nawo kumeneko. Chifukwa cha zochita zawo zoipa, ndidzawathamangitsa panyumba yanga.+ Ndipo sindidzawakondanso.+Akalonga awo onse ndi amakani. Amosi 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ‘Bwerani ku Beteli anthu inu kuti mudzachite zolakwa,*+Bwerani ku Giligala kuti mudzawonjezere machimo.+ Bweretsani nsembe zanu+ mʼmawa.Ndipo pa tsiku lachitatu, mubweretse chakhumi* chanu.+
15 “Zoipa zawo zonse zinachitikira ku Giligala,+ ndipo ndinadana nawo kumeneko. Chifukwa cha zochita zawo zoipa, ndidzawathamangitsa panyumba yanga.+ Ndipo sindidzawakondanso.+Akalonga awo onse ndi amakani.
4 ‘Bwerani ku Beteli anthu inu kuti mudzachite zolakwa,*+Bwerani ku Giligala kuti mudzawonjezere machimo.+ Bweretsani nsembe zanu+ mʼmawa.Ndipo pa tsiku lachitatu, mubweretse chakhumi* chanu.+