Yoswa 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova Mulungu wathu ndi amene anatitulutsa mʼdziko la Iguputo pamodzi ndi makolo athu,+ kutichotsa kudziko lomwe tinali akapolo.+ Iye anachita zizindikiro zazikulu pamaso pathu+ ndi kutiteteza njira yonse. Anatitetezanso kwa anthu onse amene tinadutsa pakati pawo.+ 1 Samueli 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yakobo atangofika ku Iguputo,+ makolo anu nʼkuyamba kupempha Yehova kuti awathandize,+ Yehova anatumiza Mose+ ndi Aroni kuti atsogolere makolo anu pochoka ku Iguputo kuti azikhala mʼdzikoli.+
17 Yehova Mulungu wathu ndi amene anatitulutsa mʼdziko la Iguputo pamodzi ndi makolo athu,+ kutichotsa kudziko lomwe tinali akapolo.+ Iye anachita zizindikiro zazikulu pamaso pathu+ ndi kutiteteza njira yonse. Anatitetezanso kwa anthu onse amene tinadutsa pakati pawo.+
8 Yakobo atangofika ku Iguputo,+ makolo anu nʼkuyamba kupempha Yehova kuti awathandize,+ Yehova anatumiza Mose+ ndi Aroni kuti atsogolere makolo anu pochoka ku Iguputo kuti azikhala mʼdzikoli.+