-
Ezekieli 33:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 “Iwe mwana wa munthu, lankhula ndi anthu a mtundu wako+ ndipo uwauze kuti,
‘Tiyerekeze kuti ndabweretsa lupanga mʼdziko,+ ndiyeno anthu onse amʼdzikolo asankha munthu kuti akhale mlonda wawo, 3 ndiye mlondayo waona lupanga likubwera kudzaukira dzikolo, nʼkuliza lipenga la nyanga ya nkhosa kuchenjeza anthu.+
-
-
Amosi 3:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Lipenga la nyanga ya nkhosa likalira mumzinda, kodi anthu sanjenjemera?
Kodi tsoka likagwa mumzinda, si Yehova amene wachititsa?
-