Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Zefaniya 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tsiku lalikulu la Yehova lili pafupi.+

      Lili pafupi ndipo likubwera mofulumira kwambiri.+

      Mkokomo wa tsiku la Yehova ukubwera ndi zowawa.+

      Pa tsiku limenelo msilikali adzalira.+

  • Zefaniya 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Tsiku loliza lipenga ndiponso la mfuu yankhondo,+

      Pochenjeza mizinda ya mipanda yolimba komanso nsanja zazitali zamʼmakona.+

  • Malaki 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Taonani! Tsiku loyaka ngati ngʼanjo likubwera,+ ndipo anthu onse odzikuza ndi onse ochita zoipa adzakhala ngati mapesi. Pa tsikulo iwo adzawonongedwa moti sipadzatsala mizu kapena nthambi zawo,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena