Zefaniya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsiku limenelo ndi tsiku la mkwiyo,+Tsiku la masautso ndi zowawa,+Tsiku lowononga ndi la mphepo yamkuntho,Tsiku la mdima wochititsa mantha,+Tsiku la mitambo ndi la mdima wandiweyani,+
15 Tsiku limenelo ndi tsiku la mkwiyo,+Tsiku la masautso ndi zowawa,+Tsiku lowononga ndi la mphepo yamkuntho,Tsiku la mdima wochititsa mantha,+Tsiku la mitambo ndi la mdima wandiweyani,+