Yoweli 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pali mtundu umene walowa mʼdziko langa, wamphamvu ndiponso wa anthu osawerengeka.+ Mano ndiponso nsagwadwa zawo zili ngati za mikango.+
6 Pali mtundu umene walowa mʼdziko langa, wamphamvu ndiponso wa anthu osawerengeka.+ Mano ndiponso nsagwadwa zawo zili ngati za mikango.+