Chivumbulutso 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Dzombelo linkaoneka ngati mahatchi okonzekera nkhondo.+ Pamitu pawo panali zinthu zooneka ngati zisoti zachifumu zagolide. Nkhope zawo zinali ngati nkhope za anthu,
7 Dzombelo linkaoneka ngati mahatchi okonzekera nkhondo.+ Pamitu pawo panali zinthu zooneka ngati zisoti zachifumu zagolide. Nkhope zawo zinali ngati nkhope za anthu,