Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 30:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Mayo ine! Chifukwa tsiku limenelo lidzakhala lochititsa mantha.*+

      Ndipo palibe lofanana nalo.

      Tsiku limenelo lidzakhala lamavuto kwa Yakobo.

      Koma adzapulumutsidwa mʼmavuto amenewa.

  • Amosi 5:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 ‘Tsoka kwa anthu amene akulakalaka tsiku la Yehova!+

      Kodi chidzakuchitikireni nʼchiyani pa tsiku la Yehova?+

      Limeneli lidzakhala tsiku lamdima, osati kuwala.+

  • Zefaniya 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Tsiku limenelo ndi tsiku la mkwiyo,+

      Tsiku la masautso ndi zowawa,+

      Tsiku lowononga ndi la mphepo yamkuntho,

      Tsiku la mdima wochititsa mantha,+

      Tsiku la mitambo ndi la mdima wandiweyani,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena