Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Yehova wanena kuti: “Ngati ungabwerere, iwe Isiraeli,

      Ngati ungabwerere kwa ine

      Ndipo ngati ungachotse mafano ako onyansa pamaso panga,

      Sudzakhalanso moyo wothawathawa.+

  • Hoseya 12:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 “Choncho bwerera kwa Mulungu wako.+

      Uzisonyeza chikondi chokhulupirika ndi chilungamo,+

      Ndipo nthawi zonse uziyembekezera Mulungu wako.

  • Hoseya 14:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Inu Aisiraeli, bwererani kwa Yehova Mulungu wanu,+

      Popeza mwapunthwa chifukwa cha zolakwa zanu.

       2 Bwererani kwa Yehova ndi mawu amenewa.

      Uzani Mulungu kuti, ‘Tikhululukireni zolakwa zathu.+ Landirani zinthu zathu zabwino,

      Ndipo tidzakutamandani ndi pakamwa pathu+ ngati mmene tingaperekere nsembe kwa inu ana a ngʼombe amphongo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena