-
Salimo 79:9, 10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Tithandizeni inu Mulungu amene mumatipulumutsa,+
Chifukwa cha dzina lanu laulemerero.
Tipulumutseni komanso mutikhululukire* machimo athu chifukwa cha dzina lanu.+
10 Musalole kuti anthu a mitundu ina azinena kuti: “Mulungu wawo ali kuti?”+
Anthu a mitundu ina adziwe ife tikuona
Kuti mwabwezera magazi a atumiki anu amene anakhetsedwa.+
-