Levitiko 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndidzakugwetserani mvula pa nthawi yake.+ Nthaka idzakupatsani chakudya,+ ndipo mitengo yamʼmunda idzakupatsani zipatso zake. Deuteronomo 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ndidzakupatsaninso mvula pa nthawi yake mʼdziko lanu, mvula yoyambirira ndi mvula yomaliza, ndipo mudzakolola mbewu zanu nʼkukhala ndi vinyo watsopano komanso mafuta.+
4 ndidzakugwetserani mvula pa nthawi yake.+ Nthaka idzakupatsani chakudya,+ ndipo mitengo yamʼmunda idzakupatsani zipatso zake.
14 ndidzakupatsaninso mvula pa nthawi yake mʼdziko lanu, mvula yoyambirira ndi mvula yomaliza, ndipo mudzakolola mbewu zanu nʼkukhala ndi vinyo watsopano komanso mafuta.+