Yoweli 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zinthu zimene ziwala zowononga zinasiya zinadyedwa ndi dzombe lambirimbiri.+Zimene dzombelo linasiya zinadyedwa ndi ana a dzombe opanda mapiko.Ndipo zimene ana a dzombe opanda mapiko anasiya zinadyedwa ndi dzombe losakaza.+
4 Zinthu zimene ziwala zowononga zinasiya zinadyedwa ndi dzombe lambirimbiri.+Zimene dzombelo linasiya zinadyedwa ndi ana a dzombe opanda mapiko.Ndipo zimene ana a dzombe opanda mapiko anasiya zinadyedwa ndi dzombe losakaza.+