Yesaya 32:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mpaka mzimu utatsanulidwa pa ife kuchokera kumwamba,+Ndiponso chipululu chitakhala munda wa zipatso,Komanso munda wa zipatsowo utayamba kuoneka ngati nkhalango.+ Yesaya 44:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa ndidzapatsa madzi munthu waludzu*+Ndipo ndidzaika timitsinje tamadzi oyenda pamalo ouma. Ndidzatsanulira mzimu wanga pa ana ako*+Komanso madalitso anga pa mbadwa zako. Ezekieli 39:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Sindidzawabisiranso nkhope yanga+ chifukwa panyumba ya Isiraeli ndidzatsanulirapo mzimu wanga,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
15 Mpaka mzimu utatsanulidwa pa ife kuchokera kumwamba,+Ndiponso chipululu chitakhala munda wa zipatso,Komanso munda wa zipatsowo utayamba kuoneka ngati nkhalango.+
3 Chifukwa ndidzapatsa madzi munthu waludzu*+Ndipo ndidzaika timitsinje tamadzi oyenda pamalo ouma. Ndidzatsanulira mzimu wanga pa ana ako*+Komanso madalitso anga pa mbadwa zako.
29 Sindidzawabisiranso nkhope yanga+ chifukwa panyumba ya Isiraeli ndidzatsanulirapo mzimu wanga,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”