-
1 Mafumu 18:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Ahabu atangoona Eliya, anati: “Kodi ndiwe eti? Iwe ndi amene wabweretsa mavuto ambiri mu Isiraeli.”
-
-
1 Mafumu 22:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Mfumu ya Isiraeli inayankha Yehosafati kuti: “Patsala munthu mmodzi amene tingathe kufunsira kwa Yehova+ kudzera mwa iye, koma ndimadana naye kwambiri,+ chifukwa salosera zabwino zokhudza ine, koma zoipa zokhazokha.+ Dzina lake ndi Mikaya mwana wa Imula.” Koma Yehosafati anati: “Mfumu siyenera kulankhula choncho.”
-