Mika 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo amalakalaka minda ya anthu ena ndipo amaitenga.+Amalakalakanso nyumba za anthu ena nʼkuzitenga.Amatenga mwachinyengo nyumba ya munthu,+Ndipo amatenganso cholowa cha munthu.
2 Iwo amalakalaka minda ya anthu ena ndipo amaitenga.+Amalakalakanso nyumba za anthu ena nʼkuzitenga.Amatenga mwachinyengo nyumba ya munthu,+Ndipo amatenganso cholowa cha munthu.