Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 74:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Kulibe zizindikiro zathu zoti tizione.

      Kulibenso mneneri wina aliyense amene watsala,

      Ndipo pakati pathu palibe amene akudziwa kuti zimenezi zikhala chonchi kwa nthawi yayitali bwanji.

  • Ezekieli 7:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Mʼdzikolo mudzakhala mavuto otsatizanatsatizana ndipo muzidzamveka mauthenga otsatizanatsatizana. Anthu azidzafuna kumva masomphenya kuchokera kwa mneneri.+ Koma wansembe sadzathanso kuphunzitsa malamulo* aphindu ndipo anthu achikulire sadzaperekanso malangizo othandiza.+

  • Mateyu 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma iye anayankha kuti, “Malemba amati: ‘Munthu sangakhale ndi moyo ndi chakudya chokha, koma ndi mawu alionse ochokera mʼkamwa mwa Yehova.’”*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena