Yeremiya 48:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chiweruzo chafika padziko lafulati.*+ Chafika ku Holoni, Yahazi,+ Mefaata,+ Yeremiya 48:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kerioti,+ Bozira ndi mizinda yonse yamʼdziko la Mowabu, yakutali ndi yapafupi.