Hoseya 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngakhale kuti inu Aisiraeli mukuchita chiwerewere,+Yuda asakhale ndi mlandu.+ Musabwere ku Giligala+ kapena ku Beti-aveni,+Ndipo musalumbire kuti, ‘Mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo!’+ Amosi 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ‘Bwerani ku Beteli anthu inu kuti mudzachite zolakwa,*+Bwerani ku Giligala kuti mudzawonjezere machimo.+ Bweretsani nsembe zanu+ mʼmawa.Ndipo pa tsiku lachitatu, mubweretse chakhumi* chanu.+
15 Ngakhale kuti inu Aisiraeli mukuchita chiwerewere,+Yuda asakhale ndi mlandu.+ Musabwere ku Giligala+ kapena ku Beti-aveni,+Ndipo musalumbire kuti, ‘Mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo!’+
4 ‘Bwerani ku Beteli anthu inu kuti mudzachite zolakwa,*+Bwerani ku Giligala kuti mudzawonjezere machimo.+ Bweretsani nsembe zanu+ mʼmawa.Ndipo pa tsiku lachitatu, mubweretse chakhumi* chanu.+