-
Yesaya 43:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Ndikumbutse, tiye tiimbane mlandu.
Fotokoza mbali yako kuti usonyeze kuti ndiwe wosalakwa.
-
-
Yeremiya 2:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Koma iwe ukunena kuti, ‘Ine ndilibe mlandu uliwonse.
Ndithudi mkwiyo wake wandichokera.’
Tsopano ndikukupatsa chiweruzo
Chifukwa ukunena kuti, ‘Sindinachimwe.’
-