Zefaniya 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye adzaloza dzanja lake kumpoto ndipo adzawononga Asuri.Adzachititsa Nineve kukhala bwinja,+ kukhala dziko louma ngati chipululu.
13 Iye adzaloza dzanja lake kumpoto ndipo adzawononga Asuri.Adzachititsa Nineve kukhala bwinja,+ kukhala dziko louma ngati chipululu.