Yesaya 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anafuula mwamphamvu ngati kubangula kwa mkango kuti: “Inu Yehova, ine ndimaimirira tsiku lonse pansanja ya mlonda,Ndipo usiku uliwonse ndimakhala pamalo anga olonderapo.+ Mika 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma ine ndidzayembekezera Yehova.+ Ndidzayembekezera moleza mtima Mulungu wa chipulumutso changa.+ Mulungu wanga adzandimvera.+
8 Kenako anafuula mwamphamvu ngati kubangula kwa mkango kuti: “Inu Yehova, ine ndimaimirira tsiku lonse pansanja ya mlonda,Ndipo usiku uliwonse ndimakhala pamalo anga olonderapo.+
7 Koma ine ndidzayembekezera Yehova.+ Ndidzayembekezera moleza mtima Mulungu wa chipulumutso changa.+ Mulungu wanga adzandimvera.+