Yesaya 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 mudzanena mwambi uwu wonyoza mfumu ya Babulo: “Amene ankagwiritsa ntchito anzake mokakamiza uja wawonongedwa! Kuponderezedwa kuja kwatha ndithu!+
4 mudzanena mwambi uwu wonyoza mfumu ya Babulo: “Amene ankagwiritsa ntchito anzake mokakamiza uja wawonongedwa! Kuponderezedwa kuja kwatha ndithu!+