-
Yesaya 14:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Sudzaikidwa mʼmanda limodzi ndi mafumuwo,
Chifukwa unawononga dziko lako lomwe,
Unapha anthu ako omwe.
Mayina a ana a anthu ochita zoipa sadzatchulidwanso.
-