Yesaya 40:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mmisiri amapanga fano lachitsulo,*Mmisiri wina wa zitsulo amachikuta ndi golide,+Ndipo amachipangira matcheni asiliva. Yesaya 46:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pali anthu amene amakhuthula golide mʼzikwama zawo.Amayeza siliva pasikelo. Iwo amalemba ganyu mmisiri wa zitsulo ndipo amapanga mulungu ndi zinthu zimenezi.+ Kenako anthuwo amayamba kumuweramira ndi kumulambira.*+
19 Mmisiri amapanga fano lachitsulo,*Mmisiri wina wa zitsulo amachikuta ndi golide,+Ndipo amachipangira matcheni asiliva.
6 Pali anthu amene amakhuthula golide mʼzikwama zawo.Amayeza siliva pasikelo. Iwo amalemba ganyu mmisiri wa zitsulo ndipo amapanga mulungu ndi zinthu zimenezi.+ Kenako anthuwo amayamba kumuweramira ndi kumulambira.*+