Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Chifukwa nyumba ya Isiraeli ndi munda wa mpesa wa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.+

      Amuna a ku Yuda ndi mitengo ya mpesa imene ankaikonda kwambiri.

      Iye ankayembekezera chilungamo,+

      Koma pankachitika zinthu zopanda chilungamo.

      Ankayembekezera zinthu zolungama

      Koma ankangomva anthu akulira chifukwa chozunzidwa.”+

  • Yeremiya 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti:

      “Dulani mitengo kuti timange malo okwera oti timenyerepo nkhondo ndi Yerusalemu.+

      Yerusalemu ndi mzinda umene ukuyenera kuimbidwa mlandu.

      Mkati mwake muli kuponderezana kokhakokha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena