Yesaya 29:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova wanena kuti: “Anthu awa amandiyandikira ndi pakamwa pawo pokhaNdipo amandilemekeza ndi milomo yawo yokha,+Koma mitima yawo aiika kutali ndi ine,Ndiponso amandiopa chifukwa cha malamulo a anthu amene anaphunzitsidwa.+
13 Yehova wanena kuti: “Anthu awa amandiyandikira ndi pakamwa pawo pokhaNdipo amandilemekeza ndi milomo yawo yokha,+Koma mitima yawo aiika kutali ndi ine,Ndiponso amandiopa chifukwa cha malamulo a anthu amene anaphunzitsidwa.+