Mika 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma iwe nsanja ya gulu la nkhosa,Malo okwera a mwana wamkazi wa Ziyoni,*+Ulamuliro udzabwerera. Ulamuliro woyamba udzabwerera kwa iwe,+Ufumu wa mwana wamkazi wa Yerusalemu.*+
8 Koma iwe nsanja ya gulu la nkhosa,Malo okwera a mwana wamkazi wa Ziyoni,*+Ulamuliro udzabwerera. Ulamuliro woyamba udzabwerera kwa iwe,+Ufumu wa mwana wamkazi wa Yerusalemu.*+