Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mika 7:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mdani wanga adzaonanso zimenezi,

      Ndipo manyazi adzagwira amene ankandinena kuti:

      “Yehova Mulungu wako ali kuti?”+

      Maso anga adzamuyangʼana.

      Iye adzapondedwapondedwa ngati matope amumsewu.

  • Zekariya 2:8, 9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Atapatsidwa ulemerero, Mulungu wandituma kwa anthu a mitundu ina amene ankakulandani zinthu zanu,+ chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Amene akukukhudzani, akukhudza mwana wa diso langa.+ 9 Ine ndidzawaloza mowaopseza, ndipo adzatengedwa ndi akapolo awo kuti akhale chuma cha akapolowo.’+ Mudzadziwa ndithu kuti Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wandituma.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena