Yoweli 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Yehova adzachitira nsanje dziko lake,Ndipo adzachitira chifundo anthu ake.+ Zekariya 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno mngelo amene ankalankhula nane uja anandiuza kuti: “Fuula kuti, ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Ndatsimikiza mtima kuti nditeteze Yerusalemu ndi Ziyoni.+
14 Ndiyeno mngelo amene ankalankhula nane uja anandiuza kuti: “Fuula kuti, ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Ndatsimikiza mtima kuti nditeteze Yerusalemu ndi Ziyoni.+