-
Yesaya 65:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 “Kumeneko sikudzakhalanso mwana wakhanda amene adzangokhala ndi moyo masiku ochepa okha,
Kapena munthu wachikulire amene sadzakwanitsa zaka zimene munthu amafunika kukhala ndi moyo.
Chifukwa aliyense amene adzamwalire ali ndi zaka 100 adzaonedwa ngati kamnyamata,
Ndipo wochimwa adzatembereredwa, ngakhale atakhala ndi zaka 100.*
-