Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 30:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kwa iwo kudzamveka mawu oyamikira ndi phokoso la kuseka kwa anthu.+

      Ndidzawachulukitsa moti sadzakhala ochepa.+

      Ndidzawachititsa kuti akhale ambiri,*

      Ndipo sadzakhala anthu ochepa.+

  • Yeremiya 31:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Choncho ndidzakumanganso ndipo udzakhalanso mtundu,+

      Iwe namwali wa Isiraeli, udzanyamulanso maseche ako

      Nʼkupita kukavina mosangalala.*+

  • Yeremiya 31:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “Taonani! Masiku akubwera, pamene ndidzachititsa kuti nyumba ya Isiraeli ndi nyumba ya Yuda ikhalenso ndi anthu ochuluka komanso ziweto zambiri,” akutero Yehova.+

  • Zekariya 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mngeloyo anauza mnzakeyo kuti: “Thamanga ukauze mnyamata uyo kuti, ‘“Mu Yerusalemu anthu azidzakhalamo+ ngati mzinda wopanda mpanda chifukwa cha anthu onse ndiponso ziweto zimene zili mmenemo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena