Salimo 107:2, 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu amene Yehova anawawombola anene zimenezi,Anthu amene anawawombola mʼmanja mwa mdani,*+ 3 Anthu amene anawasonkhanitsa pamodzi kuchokera mʼmayiko osiyanasiyana,+Kuchokera kumʼmawa komanso kumadzulo,*Kuchokera kumpoto komanso kumʼmwera.+
2 Anthu amene Yehova anawawombola anene zimenezi,Anthu amene anawawombola mʼmanja mwa mdani,*+ 3 Anthu amene anawasonkhanitsa pamodzi kuchokera mʼmayiko osiyanasiyana,+Kuchokera kumʼmawa komanso kumadzulo,*Kuchokera kumpoto komanso kumʼmwera.+