Yeremiya 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pa nthawi imeneyo mzinda wa Yerusalemu adzautchula kuti mpando wachifumu wa Yehova.+ Ndipo mitundu yonse adzaisonkhanitsa pamodzi ku Yerusalemu kuti ikatamande dzina la Yehova+ kumeneko. Iwo sadzaumitsanso khosi nʼkumatsatira mitima yawo yoipayo. Yoweli 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma ku Yuda kuzidzakhala anthu nthawi zonse,Ndipo ku Yerusalemu kudzakhala anthu mibadwomibadwo.+ Amosi 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzasonkhanitsa ndi kubwezeretsa anthu anga Aisiraeli amene anatengedwa kupita ku ukapolo.+Iwo adzamanga mizinda imene ili yabwinja nʼkumakhalamo.+Adzalima minda ya mpesa nʼkumwa vinyo wake.+Adzalimanso minda nʼkudya zipatso zake.’+
17 Pa nthawi imeneyo mzinda wa Yerusalemu adzautchula kuti mpando wachifumu wa Yehova.+ Ndipo mitundu yonse adzaisonkhanitsa pamodzi ku Yerusalemu kuti ikatamande dzina la Yehova+ kumeneko. Iwo sadzaumitsanso khosi nʼkumatsatira mitima yawo yoipayo.
20 Koma ku Yuda kuzidzakhala anthu nthawi zonse,Ndipo ku Yerusalemu kudzakhala anthu mibadwomibadwo.+
14 Ndidzasonkhanitsa ndi kubwezeretsa anthu anga Aisiraeli amene anatengedwa kupita ku ukapolo.+Iwo adzamanga mizinda imene ili yabwinja nʼkumakhalamo.+Adzalima minda ya mpesa nʼkumwa vinyo wake.+Adzalimanso minda nʼkudya zipatso zake.’+