Hagai 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwadzala mbewu zambiri, koma mukukolola zochepa.+ Mukudya, koma simukukhuta. Mukumwa koma simukukhutira. Mukuvala zovala, koma simukumva kutenthera. Ndipo amene akugwira ganyu akuika ndalama zake mʼmatumba obowoka.’”
6 Mwadzala mbewu zambiri, koma mukukolola zochepa.+ Mukudya, koma simukukhuta. Mukumwa koma simukukhutira. Mukuvala zovala, koma simukumva kutenthera. Ndipo amene akugwira ganyu akuika ndalama zake mʼmatumba obowoka.’”