Hagai 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kodi mbewu zilipobe mʼnyumba yosungiramo mbewu?*+ Kodi mitengo ya mpesa, ya mkuyu, ya makangaza* ndi ya maolivi yabereka zipatso? Kuyambira lero ndikupatsani madalitso.’”+
19 Kodi mbewu zilipobe mʼnyumba yosungiramo mbewu?*+ Kodi mitengo ya mpesa, ya mkuyu, ya makangaza* ndi ya maolivi yabereka zipatso? Kuyambira lero ndikupatsani madalitso.’”+